Ministry Assistant 2
Ya mipingo

Mpingo wanu wonse mu pulogilamu imodzi

Mapulogilamu a misonkhano, nchito zopatsidwa, ulaliki wapoyela, magawo na malipoti a tumagulu - zogaŵanidwa na wofalitsa aliyense ndipo zobisidwa kucokela mbali imodzi kufika ina.

Posacedwa

Zinthu za mpingo zikubwela mu mtundu wotsatila wa pulogilamu. Zonse za utumiki wanu waumwini zakonzeka ndipo mungazigwilitse nchito kwaulele lelo.