Kukumana kokonzekela ulaliki
Ndandanda ya kukumana kokonzekela ulaliki kwa mpingo na gulu lililonse la ulaliki.
Vidiyoyi ili mu Cingelezi. Masitepe ali pansipa amafotokoza zomwezo mu cinenelo canu.
Sitepe na sitepe
Ndandanda
Pano pali ndandanda ya kukumana kokonzekela ulaliki: kwa mpingo wonse na kwa gulu lililonse la ulaliki.
Onjezelani kukumana
Dinizani Onjezelani kukumana ndipo sankhani tsiku na nthawi, kwa ndani na malo. Kukumana kungabwelele mlungu uliwonse kapena kuchitika kamodzi kokha.
Amene amatsogoza
Pa kukumana kwa mlungu uliwonse, wotsogoza amasankhidwa pa tsiku lililonse mu mndandanda wa kukumana kotsatila.
Mfundo za kukumana
Tsegulani kukumana kuti muone wotsogoza, malo na malangizo pa mapu na magawo a tsikulo.
Kukumana kwa magulu
Oyang’anila magulu na othandiza awo amakonza apa kukumana kwa gulu lawo.